Search Results
See All Results
Home
Groups
Pages
See More
Groups
Pages
Events
Blogs
Offers
Jobs
Courses
Forums
Movies
Games
About
Terms
Privacy
Join
Sign In
Sign Up
Theme Switcher
Night Mode
Search
Posts
Blogs
Users
Pages
Groups
Events
Jadim Jadim
@Jadim
added blog in
Other
2025-01-05 13:45:59
Mayi Mary Laini Kaude azaka 87 ochokera m'mudzi wa Matewere mdera la mfumu yayikulu Juma m'boma la Mulanje ali mu ululu
Mayi Mary Laini Kaude azaka 87 ochokera m'mudzi wa Matewere mdera la mfumu yayikulu Juma m'boma la Mulanje ali mu ululu pomwe anthu okwiya anawamenya usiku wa lachinayi sabata ino ati powaganizira kuti akumanga mvula. A Catherine Namanya omwe ndi mdzukulu wa mayiwa ati anthuwa analowa m'nyumba ya mayiwa kudzera pa zenera ndikuyamba kuwagenda. Iwo ati anthu ena oyandikira atamva...
3
·
0 Comments
·
0 Shares
·
298 Views
·
0 Reviews
Please log in to like, share and comment!