Mayi Mary Laini Kaude azaka 87 ochokera m'mudzi wa Matewere mdera la mfumu yayikulu Juma m'boma la Mulanje ali mu ululu

0
638
Mayi Mary Laini Kaude azaka 87 ochokera m'mudzi wa Matewere mdera la mfumu yayikulu Juma m'boma la Mulanje ali mu ululu pomwe anthu okwiya anawamenya usiku wa lachinayi sabata ino ati powaganizira kuti akumanga mvula.
A Catherine Namanya omwe ndi mdzukulu wa mayiwa ati anthuwa analowa m'nyumba ya mayiwa kudzera pa zenera ndikuyamba kuwagenda.
Iwo ati anthu ena oyandikira atamva phokoso la anthuwa anathamangira kunyumbayo komwe anawapulumutsa ndikuwatengela ku chipatala chaching'ono cha Namphungo ndipo anawatumiza kuchipatala chachikulu cha bomali komwe anawagoneka kwa masiku awiri akulandira thandizo.
Pakadali pano m'neneri wa apolisi m'bomali Innocent Moses wati timupase nthawi asanaikepo ndemanga pa nkhaniyi.
Polakhula ndi mkulu wa bungwe lomenyera ufulu wa anthu achikulire m'dziko muno la MANEPO a Andrew Kavala apempha apolisi kufufuza zankhaniyi ndikuonesetsa kuti malamulo agwira ntchito kwa anthu omwe anachita zaupanduzi.
Wolemba :Grecium Gama
Sad
3
Αναζήτηση
Κατηγορίες
Διαβάζω περισσότερα
Food
The Rising Popularity of Mustard Oil: Exploring Prices in Pakistan
Mustard oil has long been a staple in many South Asian kitchens, prized for its distinct flavor...
από Saad Afzal 2024-11-02 15:25:04 0 559
Crafts
Maximize Product Safety with POF Shrink Film
As a trusted POF shrink film manufacturer, JT Package offers premium polyolefin shrink films...
από Jiang000 Jiang000 2025-04-01 03:58:42 0 268
Crafts
Top Choice POF Shrink Film for Businesses
When it comes to packaging products securely and efficiently, pof film shrink offers a...
από Jiang000 Jiang000 2025-04-03 02:13:58 0 249
Music
Malinga - Bachelor of Arts EP 📂 27 December 2024!!
Malinga - Bachelor of Arts EP 27 December 2024!! Big S/O to Producers/ Engineers: Dj Sley,...
από palvibe 2024-12-21 10:13:52 0 569
άλλο
ノートパソコンを常に電源に接続したままにしておいても大丈夫ですか?バッテリーにダメージを与えますか?
日常生活でノートパソコンを使用する場合、多くのユーザーは「ノートパソコンは常に電源に接続しておくべきなのか?」という疑問に悩まされます。バッテリーを長時間接続したままにしておくとバッテリーが損傷...
από Batteryprojp Fujitsubattery 2025-04-18 04:28:11 0 70